Speed Fitment and Service Centre

Call Directions Website Contact the business

Speed Fitment and Service Centre We're a motor vehicle company offering quality car fitment & service for all vehicle types in Malawi.
(1)

10/10/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Gabriel Gfo Folomani, Pirirani Chavula, Jackson Maston, Chifuniro Chipendo, Christina Naitanda, Troubleh Chikopa, Thandeka Kamwendo, Esthear Wachisomo Joshua, Mac Donald Maunde, Sal Rahma, Treymos Saidi, Angella Chakwawa, Carlo Pinanji, Mphaa Tso, Naomi Magola, Symon Makabila Longwe, Agness Nyirenda

Dzuwa lija ndiye latuluka lokha mmadela ambiri, tidziwe nawo dela lanu ngati latuluka dzuwali tiyambepo Programme yaku n...
07/10/2026

Dzuwa lija ndiye latuluka lokha mmadela ambiri, tidziwe nawo dela lanu ngati latuluka dzuwali tiyambepo Programme yaku nyanja molingana ndi dela lomwe tili ndi ⭐⭐⭐ Star Coaches...

Company yachitatu yomwe ili pansi pa Speed Fitment and service centre ndi Speed tippers.tiwuzeni chilichonsecho tikanyam...
03/10/2026

Company yachitatu yomwe ili pansi pa Speed Fitment and service centre ndi Speed tippers.

tiwuzeni chilichonsecho tikanyamula

Speed Tippers
Anything is lighter with us

Birthday ya Speed yayenda bwino in all our Service centres.Lilongwe and Mzuzu ma results ndi amenewa tikudikirira Blanty...
01/10/2026

Birthday ya Speed yayenda bwino in all our Service centres.

Lilongwe and Mzuzu ma results ndi amenewa tikudikirira Blantyre ndipo tinene awawa ndi ma official results a momwe Birthday yayendera and ma customer athu anjoyaso lero...

Amene simunabwere Lero timati tikuwuzeni kuti mawa mpaka loweluka alignment muzapangitsa pa 10,000 kwacha ina all our Service centres.

And thank you for being with us and help us to grow.

Expect more from us to you our Great Customers.

Lero pa 1 October nditsiku lomwe Speed Fitment inabadwa mu chaka cha 2019 ndipo yakwanitsa zaka 7.pokondwelera tatsitsa ...
01/10/2026

Lero pa 1 October nditsiku lomwe Speed Fitment inabadwa mu chaka cha 2019 ndipo yakwanitsa zaka 7.

pokondwelera tatsitsa mitengo ya ma tayala athu monga pachithunzipa komanso mukagula ma tayala kwa ife tizakupangilani Fitting, Balancing ndi alignment mwa ulere 🔥🔥🔥🔥

Ndipo Izi zichitika mpaka pa 1 November 2026 akasi......

Lowani mu summer ndi matayala a nyuwani kuchokera ku speed Fitment And service centre.

Happy Birthday to us 🥳🥳🥳🎂🎂🎂🎂🎂🎂🎂🎂🎂🎂

30/09/2026

Big shout out to my newest top fans! Modestar Mwanika, Marv Chirwa, Nafeh Phiri, Tricia Namanja, Amos Mkwaila, Linda Thavera, Sean Kay, Harriet Zamawe Makanjira, Emily Chikumba, Chitsanzo Daisy Khoza, Martin Phiri Wilson, Memwa Chauya, Emmanuel Zee, Hamee Sh, Ella Nkhoma, Eliza Ndalama Chitekwe, Esnart Kumanda, Vio Let, Chewazi Gideon Daniel, Yonzi Chioko, Ťãbîţhă Šhábá, Joels Mummie, Juliana Jeremia, Precious Idana, Eunice Benson, Ble Ssings, Pat Wa Mdala, Enoch Samuel, Patience Patience, Hunks Jumbe, Bexy Kanyaxy, Debbie Bwaila, Irene Lennie, Ticia Bwanali, Mamta Careen, Mary Makawa, Elizabeth Kamanga, Vanessa Chisi, Bridget Napolo, Grace N Chiukepo, Lonney Jackson, Mercy Bauleni Mandala, Grace Lundu, Mwiza Msiska, Hilda Chiwinga, Mercy Timothy, Rudo Muli Kutchire, Thoko Tembo, Muwalo Chafukila, Rissie K Nkhata

Company ina yomwe ili pansi pa Speed Fitment ndi Tripple star express, ma bus abwino komanso very Comfortable.m***a kupa...
27/09/2026

Company ina yomwe ili pansi pa Speed Fitment ndi Tripple star express, ma bus abwino komanso very Comfortable.

m***a kupanga hire mkupita kulikonseko komanso service timapanga tokha ndi osakayikitsa awa...

Kaya ndi ku church kaya ndi family kaya ndi gulu lachipereganyu kaya ndi lazibambo tiwuzeni

ndipo ma bus wa akupezeka ku Lilongwe, Mzuzu komanso Blantyre.

October yu kunyanja titani? Tipatseni plan.

Tripple Star Express
Always on the move

25/09/2026

Limodzi mwamakampani omwe ali pansi pa Speed Fitment And Service Centre ndi.......

*UPTOWN EXECUTIVE BARBERSHOP*

Ndipo BARBERSHOP zi zili Ku Mzuzu komanso Ku Blantyre pompaja pa old AXA depot.

Ndipo pakali pano aliyese opititsa galimoto for any service ali ndi mwayi okametetsa ulere ku Barbershop yobhebhayi.

Kumeneku kuli massage, pedicure komanso face scrub.

More in the Vedio....

Partner Barbershop koma iyiiiiiii

This too is Love...Tiyeni ku Page kwawo follow them And also tag them in the comment.Aku BLANTYRE lets go.....💥💥💥💥💥🔥🔥🔥
25/09/2026

This too is Love...

Tiyeni ku Page kwawo follow them And also tag them in the comment.

Aku BLANTYRE lets go.....💥💥💥💥💥🔥🔥🔥

24/09/2026

kodi mukudziwa kuti Speed Fitment iliso ndi ma company ena atatu pansi pake Partner??

khalani Tchelu muwadziwe ndipo kubhebha A partner.

🔥🔥🔥🔥🔥💥💥💥💥💥💥💥💥
Zabwino zikubwerabeeeeee

Address

Blantyre
C/O1123

Opening Hours

Monday 07:30 - 17:00
Tuesday 07:30 - 17:00
Wednesday 07:30 - 17:00
Thursday 07:30 - 17:00
Friday 07:30 - 17:00
Saturday 08:00 - 15:00

Telephone

+265991228771

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Speed Fitment and Service Centre posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Speed Fitment and Service Centre:

Shortcuts

Share