Mtendere Auto Parts

Mtendere Auto Parts Welcome to Mtendere Auto parts Suppliers of original motor Spare parts from Dubai, South Africa and UK. We.

Sell Air filter elements, spark plugs, brake pads, oil filters, diesel filters and adhesives such as glue devil and prime bond.

Izinso tili nazo. Tipezeni. Z212, Z350 and Z217 zonsezi zilipo. Tili mu Malangalanga komanso 4 ways Trading center, ku A...
03/08/2026

Izinso tili nazo. Tipezeni. Z212, Z350 and Z217 zonsezi zilipo.
Tili mu Malangalanga komanso 4 ways Trading center, ku Airwing Nseu wa Nsaru.

Asimco brake pad. Ayambira 35,000 ya Suzuki Alto. Yolimba kwambiri. No noise. Mpaka 20,000kilometers. Kupanga engine ser...
30/07/2026

Asimco brake pad. Ayambira 35,000 ya Suzuki Alto. Yolimba kwambiri. No noise. Mpaka 20,000kilometers. Kupanga engine service kangapo koma osasintha brake pad.
Tili ku Malangalanga komanso ku airwing 4 ways TC, nseu wa Nsaru.

Air filter ya GD6 m***a kuzaoda this week pa 30,000. Glue devil m***a kuzaoda pa 5,000. Mubwere week inotu koma tamvana ...
27/07/2026

Air filter ya GD6 m***a kuzaoda this week pa 30,000. Glue devil m***a kuzaoda pa 5,000. Mubwere week inotu koma tamvana ma customers eti. Changu, mungapeze zitatha. Shop paja ili ku Malangalanga. Inanso ili pa 4 ways airwing tikamapita ku Nsaru. Zikomo. Timakunyadirani kwambiri.

We have these and many more.Tili ku Malangalanga komanso pa 4 ways trading center ku airwing, nseu wa Nsaru.Tipezeni
25/07/2026

We have these and many more.
Tili ku Malangalanga komanso pa 4 ways trading center ku airwing, nseu wa Nsaru.
Tipezeni

Bearing iyiyi palibenso. Ndi mwala mwala. Mawa titsegula. Tipezeni ku Malangalanga mu Autolube building near old skyway ...
05/07/2026

Bearing iyiyi palibenso. Ndi mwala mwala. Mawa titsegula. Tipezeni ku Malangalanga mu Autolube building near old skyway College.

Katundu wina ndi ameneyu. Tipezeni ku Malangalanga mu Autolube building pafupi ndi skyway College yakale.
04/07/2026

Katundu wina ndi ameneyu. Tipezeni ku Malangalanga mu Autolube building pafupi ndi skyway College yakale.

Tili ndi izi komanso ma Plug ndi ma brake pad a Asimco. Bwerani ndithu. Order zikuthekanso GUD oil filters aliponso.
04/07/2026

Tili ndi izi komanso ma Plug ndi ma brake pad a Asimco. Bwerani ndithu. Order zikuthekanso GUD oil filters aliponso.

https://whatsapp.com/channel/0029Vb7HhMa4IBhNLOkDjD0QKindly follow our WhatsApp channel for more.
27/06/2026

https://whatsapp.com/channel/0029Vb7HhMa4IBhNLOkDjD0Q
Kindly follow our WhatsApp channel for more.

Follow Mtendere Auto Parts's WhatsApp channel. We are trusted distributors of automotive spare parts from South Africa and Dubai. We are in Malangalanga and 4 ways Trading center in Lilongwe. We send to all locations in Malawi and Lusaka in Zambia. Join 18 followers for the latest updates.

Tili mu Malangalanga mu Autolube Building pafupi ndi skyway College yakale. Komanso tili pa 4 ways trading center Nseu w...
26/06/2026

Tili mu Malangalanga mu Autolube Building pafupi ndi skyway College yakale. Komanso tili pa 4 ways trading center Nseu wa Kasiya, kudusa pa Meru filling station.
0981152015. 0998656324. 0881782509.

Address

Lilongwe

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 17:00
Thursday 09:00 - 17:00
Friday 09:00 - 17:00
Saturday 09:00 - 17:00
Sunday 09:00 - 17:00

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mtendere Auto Parts posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share